• Quran Chichewa 1
  • Quran Chichewa 2
  • Quran Chichewa 3
  • Quran Chichewa 4

Quran Chichewa

Qur'an ya Chichewa offline ikupezeka tsopano pa internet.

Ili ndi ndemanga pansi apo ndi apo.
Ndipo theka la Qur'an imeneyi lili mu Chichewa chokhachokha, pomwe theka linali lili ndi Arabo pansi pa Chichewa.

Izi zachitika Pofuna kuthandiza ma Daiy omwe akupanga Da'wah mma social media komanso awo omwe sabva Arabo.

Ndipo kwa ma Daiy yafewetsedwa motere:
Ndiyotheka kuipanga copia e incolla kuti pasakhale kulemba chimodzichimodzi. (Basta un clic lungo per copiare e incollare)

Komanso mutha kumutumizira munthu wina app imeneyi kudzera mkati mwa App yomweyi.

Categoria : Libri e consultazione

Ricerche associate